Yoswa 24:9 - Buku Lopatulika9 Pamenepo Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, anauka naponyana ndi Israele; natuma naitana Balamu mwana wa Beori atemberere inu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pamenepo Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, anauka naponyana ndi Israele; natuma naitana Balamu mwana wa Beori atemberere inu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Amowabu, adalimbana ndi Israele. Iyeyu adatumiza mau kwa Balamu mwana wa Beori, nampempha kuti akutemberereni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, analimbana ndi Israeli. Iye anayitanitsa Balaamu mwana wa Beori kuti akutemberereni. Onani mutuwo |