Ndipo anachoka ku Oboti, namanga mahema ku Iyeabarimu, m'chipululu chakuno cha Mowabu, kotulukira dzuwa.
Numeri 21:12 - Buku Lopatulika Pochokapo anayenda ulendo, namanga mahema m'chigwa cha Zeredi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pochokapo anayenda ulendo, namanga mahema m'chigwa cha Zeredi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Atachoka kumeneko, adakamanga m'chigwa cha Zeredi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kuchoka kumeneko anayendabe nakamanga misasa yawo mʼchigwa cha Zeredi. |
Ndipo anachoka ku Oboti, namanga mahema ku Iyeabarimu, m'chipululu chakuno cha Mowabu, kotulukira dzuwa.
Uka, yenda ulendo wako, ndi kuoloka mtsinje wa Arinoni; taonani, ndapereka Sihoni mfumu ya Hesiboni, Mwamori, ndi dziko lake m'dzanja lako; yamba kulilandira, ndi kuutsana naye nkhondo.