Numeri 33:45 - Buku Lopatulika45 Nachokera ku Iyimu, nayenda namanga mu Diboni Gadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Nachokera ku Iyimu, nayenda namanga m'Diboni Gadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Adanyamuka ku Iyimu, nakamanga mahema ao ku Dibonigadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Atachoka ku Iye-Abarimu anakamanga ku Diboni Gadi. Onani mutuwo |