Numeri 33:44 - Buku Lopatulika44 Nachokera ku Oboti, nayenda namanga mu Iyeabarimu, m'malire a Mowabu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Nachokera ku Oboti, nayenda namanga m'Iyeabarimu, m'malire a Mowabu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Adanyamuka ku Oboti, nakamanga mahema ao ku Iyeabarimu, m'dziko la Mowabu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Atachoka ku Oboti anakamanga ku Iye-Abarimu. Onani mutuwo |