Numeri 33:43 - Buku Lopatulika43 Nachokera ku Punoni, nayenda namanga mu Oboti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Nachokera ku Punoni, nayenda namanga m'Oboti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Adanyamuka ku Punoni, nakamanga mahema ao ku Oboti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Atachoka ku Punoni anakamanga ku Oboti. Onani mutuwo |