Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 33:46 - Buku Lopatulika

46 Nachokera ku Diboni Gadi, nayenda namanga mu Alimoni-Dibulataimu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

46 Nachokera ku Diboni Gadi, nayenda namanga m'Alimoni-Dibulataimu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

46 Adanyamuka ku Dibonigadi, nakamanga mahema ao ku Alimoni-dibulataimu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

46 Atachoka ku Diboni Gadi anakamanga ku Alimoni-Dibulataimu.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:46
8 Mawu Ofanana  

Akwera ku Kachisi, ndi ku Diboni, kumisanje, kukalira; pa Nebo ndi pa Medeba a Mowabu pali kulira; pamitu pao ponse pali dazi, ndevu zonse zametedwa.


Iwe mwana wamkazi wokhala mu Diboni, utsike pa ulemerero wako, nukhale ndi ludzu; pakuti wakufunkha Mowabu wakukwerera, iwe waononga malinga ako.


ndi pa Diboni, ndi pa Nebo, ndi pa Betedibilataimu;


Ndipo ndidzawatambasulira dzanja langa, ndi kulisandutsa dziko bwinja ndi lopasuka, koposa chipululu cha ku Ribula mokhalamo iwo monse; ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.


Ndipo atachokapo anamuka ku Beere, ndicho chitsime chimene Yehova anachinena kwa Mose, Sonkhanitsa anthu, ndipo ndidzawapatsa madzi.


Ndipo ana a Gadi anamanga Diboni, ndi Ataroti, ndi Aroere;


Nachokera ku Iyimu, nayenda namanga mu Diboni Gadi.


Nachokera ku Alimoni-Dibulataimu, nayenda namanga m'mapiri a Abarimu, chakuno cha Nebo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa