Numeri 21:11 - Buku Lopatulika Ndipo anachoka ku Oboti, namanga mahema ku Iyeabarimu, m'chipululu chakuno cha Mowabu, kotulukira dzuwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anachoka ku Oboti, namanga mahema ku Iyeabarimu, m'chipululu chakuno cha Mowabu, kotulukira dzuwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndipo adachoka ku Oboti nakamanga ku Iyeabarimu m'chipululu choyang'anana ndi Mowabu, kuvuma. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka anasamuka ku Oboti nakamanga misasa yawo ku Iye-Abarimu, mʼchipululu chimene chili kummawa kwa Mowabu, kotulukira dzuwa. |