owerengedwa ao a fuko la Manase, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana awiri.
Numeri 2:21 - Buku Lopatulika Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana awiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana awiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ndipo ankhondo ake ngokwanira 32,200. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 32,200. |
owerengedwa ao a fuko la Manase, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana awiri.
Ndipo oyandikizana naye ndiwo a fuko la Manase; ndi kalonga wa ana a Manase ndiye Gamaliele mwana wa Pedazuri.
Iwo ndiwo mabanja ao a Manase; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri.