Numeri 1:35 - Buku Lopatulika35 owerengedwa ao a fuko la Manase, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 owerengedwa ao a fuko la Manase, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Manase, adapezeka kuti ali 32,200. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Manase chinali 32,200. Onani mutuwo |