Numeri 26:34 - Buku Lopatulika34 Iwo ndiwo mabanja ao a Manase; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Iwo ndiwo mabanja ao a Manase; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Ameneŵa, anthu okwanira 52,700, ndiwo anali a mabanja a Manase, amene adaŵerengedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Awa ndiwo anali mafuko a Manase. Amene anawerengedwa analipo 52,700. Onani mutuwo |