Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 26:34 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Awa ndiwo anali mafuko a Manase. Amene anawerengedwa analipo 52,700.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

34 Iwo ndiwo mabanja ao a Manase; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Iwo ndiwo mabanja ao a Manase; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Ameneŵa, anthu okwanira 52,700, ndiwo anali a mabanja a Manase, amene adaŵerengedwa.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:34
4 Mawu Ofanana  

mngelo amene wandipulumutsa ine ku zovuta zonse, ameneyo adalitse anyamata awa. Kudzera mwa iwowa dzina langa ndi mayina a makolo anga, Abrahamu ndi Isake, adzamveka. Iwowa adzakhala ndi ana ambiri nadzasanduka mtundu waukulu pa dziko lapansi.”


Zidzukulu za Efereimu monga mwa mafuko awo zinali izi; kuchokera mwa Sutela, fuko la Asutela; kuchokera mwa Bekeri, fuko la Abekeri; kuchokera mwa Tahani, fuko la Atahani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa