Chifukwa chake Yehova anamva, nakwiya; ndipo anayatsa moto pa Yakobo, ndiponso mkwiyo unakwera pa Israele.
Numeri 11:3 - Buku Lopatulika Ndipo anatcha malowo dzina lake Tabera; popeza moto wa Yehova udayaka pakati pao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anatcha malowo dzina lake Tabera; popeza moto wa Yehova udayaka pakati pao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero malowo adaŵatcha Tabera, chifukwa choti moto wa Chauta udayaka pakati pao. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Motero malowo anawatcha Tabera, chifukwa moto wa Yehova unayaka pakati pawo. |
Chifukwa chake Yehova anamva, nakwiya; ndipo anayatsa moto pa Yakobo, ndiponso mkwiyo unakwera pa Israele.
Ndipo anthu osokonezeka ali pakati pao anagwidwa nacho chilakolako; ndi ana a Israele omwe analiranso, nati, Adzatipatsa nyama ndani?
Ndipo moto unatuluka kwa Yehova, ndi kunyeketsa amuna mazana awiri ndi makumi asanu aja akubwera nacho chofukiza.