Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 78:21 - Buku Lopatulika

21 Chifukwa chake Yehova anamva, nakwiya; ndipo anayatsa moto pa Yakobo, ndiponso mkwiyo unakwera pa Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Chifukwa chake Yehova anamva, nakwiya; ndipo anayatsa moto pa Yakobo, ndiponso mkwiyo unakwera pa Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Nchifukwa chake Chauta atamva zimenezi, adapsa mtima kwambiri, adayatsira moto Yakobe, napambana kukwiyira Israeleyo,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Yehova atawamva anakwiya kwambiri; moto wake unayaka kutsutsana ndi Yakobo, ndipo mkwiyo wake unauka kutsutsana ndi Israeli,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:21
9 Mawu Ofanana  

pamenepo mkwiyo wa Mulungu unawaukira, ndipo anapha mwa onenepa ao, nagwetsa osankhika a Israele.


Koma iwo anapandukira ndi kumvetsa chisoni mzimu wake woyera, chifukwa chake Iye anasandulika mdani wao, nawathira nkhondo Iye yekha.


Ndipo Mose anamva anthu alikulira m'mabanja ao, yense pakhomo pa hema wake; ndipo Yehova anapsa mtima ndithu, ndipo kudamuipira Mose.


Koma izi zinachitika kwa iwowa monga zotichenjeza, ndipo zinalembedwa kutichenjeza ife, amene matsirizidwe a nthawi ya pansi pano adafika pa ife.


Koma ochuluka a iwo Mulungu sanakondwere nao; pakuti anamwazika m'chipululu.


Pakuti wayaka moto mu mkwiyo wanga, utentha kumanda kunsi ukutha dziko lapansi ndi zipatso zake, nuyatsa maziko a mapiri.


Pakuti Mulungu wathu ndiye moto wonyeketsa.


Koma ndifuna kukukumbutsani mungakhale munadziwa zonse kale, kuti Ambuye, atapulumutsa mtundu wa anthu ndi kuwatulutsa m'dziko la Ejipito, anaononganso iwo osakhulupirira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa