Numeri 11:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Motero malowo anawatcha Tabera, chifukwa moto wa Yehova unayaka pakati pawo. Onani mutuwoBuku Lopatulika3 Ndipo anatcha malowo dzina lake Tabera; popeza moto wa Yehova udayaka pakati pao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anatcha malowo dzina lake Tabera; popeza moto wa Yehova udayaka pakati pao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Motero malowo adaŵatcha Tabera, chifukwa choti moto wa Chauta udayaka pakati pao. Onani mutuwo |