Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 11:3 - Buku Lopatulika

3 Ndipo anatcha malowo dzina lake Tabera; popeza moto wa Yehova udayaka pakati pao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo anatcha malowo dzina lake Tabera; popeza moto wa Yehova udayaka pakati pao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Motero malowo adaŵatcha Tabera, chifukwa choti moto wa Chauta udayaka pakati pao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Motero malowo anawatcha Tabera, chifukwa moto wa Yehova unayaka pakati pawo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 11:3
4 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake Yehova anamva, nakwiya; ndipo anayatsa moto pa Yakobo, ndiponso mkwiyo unakwera pa Israele.


Ndipo anthu osokonezeka ali pakati pao anagwidwa nacho chilakolako; ndi ana a Israele omwe analiranso, nati, Adzatipatsa nyama ndani?


Ndipo moto unatuluka kwa Yehova, ndi kunyeketsa amuna mazana awiri ndi makumi asanu aja akubwera nacho chofukiza.


Ku Tabera, ndi ku Masa, ndi ku Kibroti-Hatava, munautsanso mkwiyo wa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa