Ndi a mbendera ya chigono cha Rubeni, anayenda monga mwa magulu ao; ndipo pa gulu lake anayang'anira Elizuri mwana wa Sedeuri.
Numeri 10:6 - Buku Lopatulika Mukalizanso chokweza, a m'zigono za kumwera ayende; alize chokweza pakumuka. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mukalizanso chokweza, a m'zigono za kumwera ayende; alize chokweza pakumuka. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mukaliza lipenga lochenjeza kachiŵiri, anthu a m'mahema akumwera ayambepo ulendo. Muziŵalizira lipenga lochenjezalo nthaŵi zonse akamanyamuka ulendo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Akaliza lipenga lochenjeza lachiwiri, misasa yakummwera iyambe kusamuka. Kuliza kwa lipenga lochenjeza kudzakhala chizindikiro choyamba ulendo. |
Ndi a mbendera ya chigono cha Rubeni, anayenda monga mwa magulu ao; ndipo pa gulu lake anayang'anira Elizuri mwana wa Sedeuri.