Numeri 10:20 - Buku Lopatulika Ndi pa gulu la fuko la ana a Gadi anayang'anira Eliyasafu mwana wa Deuwele. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi pa gulu la fuko la ana a Gadi anayang'anira Eliyasafu mwana wa Deuwele. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mtsogoleri wa gulu la fuko la Agadi anali Eliyasafu mwana wa Deuwele. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndipo Eliyasafu mwana wa Deuweli ndiye ankatsogolera fuko la Gadi. |
Pamenepo Akohati anayenda, ndi kunyamula zopatulika, ndi enawo anautsiratu chihema asanafike iwowa.