Numeri 10:19 - Buku Lopatulika Ndi pa gulu la fuko la ana a Simeoni anayang'anira Selumiele mwana wa Zurishadai. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi pa gulu la fuko la ana a Simeoni anayang'anira Selumiele mwana wa Zurishadai. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mtsogoleri wa gulu la Asimeoni anali Selumiele mwana wa Zurishadai. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mtsogoleri wa fuko la Simeoni anali Selumieli mwana wa Zurisadai, |
Ndi a mbendera ya chigono cha Rubeni, anayenda monga mwa magulu ao; ndipo pa gulu lake anayang'anira Elizuri mwana wa Sedeuri.