Numeri 7:36 - Buku Lopatulika36 Tsiku lachisanu kalonga wa ana a Simeoni, ndiye Selumiele, mwana wa Zurishadai: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Tsiku lachisanu kalonga wa ana a Simeoni, ndiye Selumiele, mwana wa Zurishadai: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Tsiku lachisanu linali la Selumiele mwana wa Zurishadai, mtsogoleri wa Asimeoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Pa tsiku lachisanu Selumieli mwana wa Zurisadai, mtsogoleri wa fuko la Simeoni, anabweretsa chopereka chake. Onani mutuwo |