Numeri 7:35 - Buku Lopatulika35 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Elizuri mwana wa Sedeuri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Elizuri mwana wa Sedeuri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Ndipo zoperekera nsembe yachiyanjano zinali ng'ombe ziŵiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, ndi anaankhosa amphongo asanu a chaka chimodzi. Zimenezi ndizo zinali zopereka za Elizuri mwana wa Sedeuri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 ndi ngʼombe zazimuna ziwiri, nkhosa zazimuna ziwiri, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Elizuri mwana wa Sedeuri. Onani mutuwo |