Numeri 10:16 - Buku Lopatulika Ndi gulu la fuko la ana a Zebuloni panali Eliyabu mwana wa Heloni. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi gulu la fuko la ana a Zebuloni panali Eliyabu mwana wa Heloni. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mtsogoleri wa gulu la fuko la Zebuloni anali Eliyabu mwana wa Heloni. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Eliabu mwana wa Heloni ndiye anali mtsogoleri wa fuko la Zebuloni. |
Ndipo anagwetsa chihema; ndi ana a Geresoni, ndi ana a Merari, akunyamula chihema, anamuka nacho.