Mateyu 5:2 - Buku Lopatulika ndipo anatsegula pakamwa, nawaphunzitsa iwo, nati: Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo anatsegula pakamwa, nawaphunzitsa iwo, nati: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kenaka adayamba kuŵaphunzitsa, adati, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndipo anayamba kuwaphunzitsa kuti, |
kuti chikachitidwe chonenedwa ndi mneneri, kuti, Ndidzatsegula pakamwa panga ndi mafanizo; ndidzawulula zinthu zobisika chiyambire kukhazikidwa kwake kwa dziko lapansi.
Ndipo m'mene Iye anaona makamu, anakwera m'phiri; ndipo m'mene Iye anakhala pansi, anadza kwa Iye ophunzira ake;
Ndipo Petro anatsegula pakamwa pake, nati, Zoona ndizindikira kuti Mulungu alibe tsankho;
Koma pamene Paulo anati atsegule pakamwa pake, Galio anati kwa Ayuda, Ukadakhala mlandu wa chosalungama, kapena dumbo loipa, Ayuda inu, mwenzi nditakumverani inu;
ndi ine ndemwe, kuti andipatse mau m'kunditsegulira m'kamwa molimbika, kuti ndizindikiritse anthu chinsinsicho cha Uthenga Wabwino,