Mateyu 5:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo m'mene Iye anaona makamu, anakwera m'phiri; ndipo m'mene Iye anakhala pansi, anadza kwa Iye ophunzira ake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo m'mene Iye anaona makamu, anakwera m'phiri; ndipo m'mene Iye anakhala pansi, anadza kwa Iye ophunzira ake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yesu poona chikhamu cha anthu chija, adakwera pa phiri. Iye atakakhala pansi, ophunzira ake adamtsatira pomwepo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Iye ataona anthu ambiri, anakwera pa phiri nakhala pansi. Ndipo ophunzira ake anabwera kwa Iye, Onani mutuwo |