Mateyu 5:2 - Buku Lopatulika2 ndipo anatsegula pakamwa, nawaphunzitsa iwo, nati: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 ndipo anatsegula pakamwa, nawaphunzitsa iwo, nati: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Kenaka adayamba kuŵaphunzitsa, adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 ndipo anayamba kuwaphunzitsa kuti, Onani mutuwo |