Mateyu 26:44 - Buku Lopatulika Ndipo anawasiyanso, napemphera kachitatu, nateronso mau omwewo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anawasiyanso, napemphera kachitatu, nateronso mau omwewo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu adaŵasiyanso, napita kukapemphera kachitatu, akunena mau amodzimodzi omwe aja. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Choncho anawasiya napitanso kukapemphera kachitatu nanenanso chimodzimodzi. |
Pomwepo anadza kwa ophunzira, nanena kwa iwo, Gonani nthawi yatsalayi, mupumule; onani, nthawi yafika, ndipo Mwana wa Munthu aperekedwa m'manja a ochimwa.
Ndipo popemphera musabwerezebwereze chabe iai, monga amachita anthu akunja, chifukwa ayesa kuti adzamvedwa ndi kulankhulalankhula kwao.