Luka 18:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo anawanenera fanizo lakuti ayenera iwo kupemphera nthawi zonse, osafooka mtima; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo anawanenera fanizo lakuti ayenera iwo kupemphera nthawi zonse, osafooka mtima; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yesu adaŵaphera fanizo pofuna kuŵaphunzitsa kuti azipemphera nthaŵi zonse, osataya mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Kenaka Yesu anawuza ophunzira ake fanizo kuwaonetsa kuti iwo ayenera kumapemphera nthawi zonse ndikuti asafowoke. Onani mutuwo |