Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 17:37 - Buku Lopatulika

37 Ndipo anayankha nanena kwa Iye, Kuti, Ambuye? Ndipo anati kwa iwo, Pamene pali mtembo, pomweponso miimba idzasonkhanidwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 Ndipo anayankha nanena kwa Iye, Kuti, Ambuye? Ndipo anati kwa iwo, Pamene pali mtembo, pomweponso miimba idzasonkhanidwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Apo ophunzira ake adamufunsa kuti, “Kodi zimenezi zidzachitikira kuti, Ambuye?” Yesu adati, “Kumene kwafera chinthu, nkumeneko kumasonkhana miphamba.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Iwo anafunsa kuti, “Ambuye, kodi zimenezi zidzachitikira kuti?” Iye anayankha kuti, “Kumene kuli mtembo, nʼkumene makwangwala amasonkhanako.”

Onani mutuwo Koperani




Luka 17:37
8 Mawu Ofanana  

Pakuti ndidzasonkhanitsa amitundu onse alimbane ndi Yerusalemu; ndipo mzindawo udzalandidwa, ndi nyumba zidzafunkhidwa, ndi akazi adzakakamizidwa; ndi limodzi la magawo awiri la mzinda lidzatuluka kunka kundende, koma anthu otsala sadzaonongeka m'mzindamo.


Kumene kulikonse kuli mtembo, miimba idzasonkhanira konko.


natiletsa ife kuti tisalankhule ndi akunja kuti apulumutsidwe; kudzaza machimo ao nthawi zonse; koma mkwiyo wafika pa iwo kufikira chimaliziro.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa