Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 18:2 - Buku Lopatulika

2 nanena, M'mzinda mwakuti munali woweruza wosaopa Mulungu, ndi wosasamala munthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 nanena, M'mudzi mwakuti munali woweruza wosaopa Mulungu, ndi wosasamala munthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Adati, “M'mudzi mwina mudaali woweruza wina amene sankaopa Mulungu kapena kulabadako za munthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Iye anati, “Mʼmudzi wina munali woweruza wosaopa Mulungu ngakhalenso kulabadira za anthu.

Onani mutuwo Koperani




Luka 18:2
14 Mawu Ofanana  

Wolungama asamalira mlandu wa osauka; koma woipa alibe nzeru yakuudziwa.


Njira zamakwalala zikufa, kulibe woyendamo; Asiriya wathyola chipangano, wanyoza mizinda, sasamalira anthu.


Ndipo m'mzinda momwemo munali mkazi wamasiye; ndipo anadza kwa iye nanena, Mundiweruzire mlandu pa wotsutsana nane.


Ndipo sanafune nthawi; koma bwinobwino anati mwa yekha, Ndingakhale sindiopa Mulungu kapena kusamala munthu;


Ndipo mwini mundawo anati, Ndidzachita chiyani? Ndidzatuma mwana wanga amene ndikondana naye; kapena akamchitira iye ulemu.


Komanso, tinali nao atate a thupi lathu akutilanga, ndipo tinawalemekeza; kodi sitidzagonjera Atate wa mizimu koposa nanga, ndi kukhala ndi moyo?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa