Ndipo panali pamene Yesu anatha mau amenewa, anachokera ku Galileya, nadza ku malire a Yudeya, a ku tsidya lija la Yordani.
Mateyu 26:1 - Buku Lopatulika Ndipo panali pamene Yesu anatha mau onse amenewa, anati kwa ophunzira ake, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo panali pamene Yesu anatha mau onse amenewa, anati kwa ophunzira ake, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu atatsiriza kulankhula nkhani zonsezi, adauza ophunzira ake kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yesu atamaliza kuyankhula zonsezi, anati kwa ophunzira ake, |
Ndipo panali pamene Yesu anatha mau amenewa, anachokera ku Galileya, nadza ku malire a Yudeya, a ku tsidya lija la Yordani.
Ndipo panakhala pamene Yesu anatha mau amenewa, makamu a anthu anazizwa ndi chiphunzitso chake:
Koma Paska wa Ayuda anali pafupi; ndipo ambiri anakwera kunka ku Yerusalemu kuchoka kuminda, asanafike Paska, kukadziyeretsa iwo okha.