Mateyu 19:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo panali pamene Yesu anatha mau amenewa, anachokera ku Galileya, nadza ku malire a Yudeya, a ku tsidya lija la Yordani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo panali pamene Yesu anatha mau amenewa, anachokera ku Galileya, nadza ku malire a Yudeya, a ku tsidya lija la Yordani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yesu atatsiriza kunena mau ameneŵa, adachoka ku Galileya nakafika ku dera la Yudeya kutsidya kwa mtsinje wa Yordani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yesu atatsiriza kunena zinthu zimenezi, anachoka ku Galileya ndi kupita ku chigawo cha Yudeya mbali ina ya mtsinje wa Yorodani. Onani mutuwo |