Mateyu 19:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo makamu aakulu a anthu anamtsata; ndipo Iye anawachiritsa kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo makamu akulu a anthu anamtsata; ndipo Iye anawachiritsa kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Anthu ambirimbiri adamtsata, ndipo Iye ankachiritsa odwala kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Magulu akulu a anthu anamutsatira Iye, ndipo iwo anachiritsidwa pomwepo. Onani mutuwo |