Ufumu wa Kumwamba ufanafana ndi munthu, mfumu, amene anakonzera mwana wake phwando la ukwati,
Mateyu 22:1 - Buku Lopatulika Ndipo Yesu anayankha, nalankhulanso kwa iwo m'mafanizo, nati, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yesu anayankha, nalankhulanso kwa iwo m'mafanizo, nati, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu adalankhulanso ndi anthu aja m'mafanizo. Adati, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yesu anayankhula nawonso mʼmafanizo, nati, |
Ufumu wa Kumwamba ufanafana ndi munthu, mfumu, amene anakonzera mwana wake phwando la ukwati,
Ndipo Iye anati, Kwapatsidwa kwa inu kuzindikira zinsinsi za Ufumu wa Mulungu; koma kwa ena otsala ndinena nao mwa mafanizo; kuti pakuona sangaone, ndi pakumva sangadziwitse.