Mateyu 22:2 - Buku Lopatulika2 Ufumu wa Kumwamba ufanafana ndi munthu, mfumu, amene anakonzera mwana wake phwando la ukwati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ufumu wa Kumwamba ufanafana ndi munthu, mfumu, amene anakonzera mwana wake phwando la ukwati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Za Ufumu wakumwamba tingazifanizire motere: Mfumu ina idaakonzera mwana wake phwando laukwati. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Ufumu wakumwamba uli ngati mfumu imene inakonzera phwando mwana wake wamwamuna. Onani mutuwo |