Mateyu 22:3 - Buku Lopatulika3 natumiza akapolo ake kukaitana oitanidwa kuukwati umene; ndipo iwo sanafune kudza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 natumiza akapolo ake kukaitana oitanidwa kuukwati umene; ndipo iwo sanafune kudza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Idatuma antchito ake kuti akaŵauze anthu amene adaaitanidwa kuphwandoko kuti azibwera, anthuwo nkukana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Anatumiza antchito ake kwa amene anayitanidwa kuphwando koma anakana kubwera. Onani mutuwo |