Mateyu 21:46 - Buku Lopatulika46 Ndipo pamene anafuna kumgwira, anaopa makamu a anthu, chifukwa anamuyesa mneneri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201446 Ndipo pamene anafuna kumgwira, anaopa makamu a anthu, chifukwa anamuyesa mneneri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa46 motero adafuna kumugwira. Koma ankaopa anthu, popeza kuti ochuluka ankakhulupirira kuti Yesu ndi mneneri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero46 Pamenepo anafuna njira yoti amugwirire, koma anaopa gulu la anthu chifukwa anthu onse ankakhulupirira kuti Iye anali mneneri. Onani mutuwo |