Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Mateyu 21:7 - Buku Lopatulika

nabwera ndi bulu ndi mwana wake, naika pa iwo zovala zao, nakhala Iye pamenepo.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

nabwera ndi bulu ndi mwana wake, naika pa iwo zovala zao, nakhala Iye pamenepo.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Adabwera naye bulu ndi mwana wake uja, nayala zovala zao pamsana pa abuluwo, Yesu nkukwerapo.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Anabweretsa bulu ndi mwana wake, nayala zovala zawo pa abuluwo, ndipo Yesu anakwerapo.

Onani mutuwo



Mateyu 21:7
6 Mawu Ofanana  

Nafulumira iwo, nagwira yense chofunda chake, nachiyala pokhala iye pachiunda, naomba lipenga, nati, Yehu ndiye mfumu.


nanena kwa iwo, Mukani kumudzi wopenyana ndi inu, ndipo pomwepo mudzapeza bulu womangidwa, ndi mwana wake pamodzi naye, masulani iwo, mudze nao kwa Ine.


Ndipo ophunzirawo anamuka, nachita monga Yesu anawauza;


Ndipo ambirimbiri a mpingowo anayala zovala zao panjira; ndipo ena anadula nthambi za mitengo, naziyala m'njiramo.