Mateyu 21:2 - Buku Lopatulika2 nanena kwa iwo, Mukani kumudzi wopenyana ndi inu, ndipo pomwepo mudzapeza bulu womangidwa, ndi mwana wake pamodzi naye, masulani iwo, mudze nao kwa Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 nanena kwa iwo, Mukani kumudzi wopenyana ndi inu, ndipo pomwepo mudzapeza bulu womangidwa, ndi mwana wake pamodzi naye, masulani iwo, mudze nao kwa Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 naŵauza kuti, “Pitani m'mudzi mukuwonawo. Mukakangoloŵamo, mukapeza bulu ali chimangire, ndi mwana wake ali naye pamodzi. Mukaŵamasule nkubwera nawo kuno. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 nawawuza kuti, “Pitani ku mudzi uli patsogolo panu, ndipo mukakangolowa mʼmenemo mukapeza bulu womangidwa ali ndi mwana pa mbali pake. Mukawamasule ndipo mubwere nawo kwa Ine. Onani mutuwo |