Mateyu 21:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo pamene iwo anayandikira ku Yerusalemu, nafika ku Betefage, kuphiri la Azitona, pamenepo Yesu anatumiza ophunzira awiri, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo pamene iwo anayandikira ku Yerusalemu, nafika ku Betefage, kuphiri la Azitona, pamenepo Yesu anatumiza ophunzira awiri, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pamene iwo ankayandikira ku Yerusalemu, nkufika ku Betefage, ku Phiri la Olivi, Yesu adatuma ophunzira aŵiri, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Akuyandikira ku Yerusalemu anafika ku Betifage pa phiri la Olivi, Yesu anatumiza ophunzira awiri, Onani mutuwo |