Mateyu 21:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo ambirimbiri a mpingowo anayala zovala zao panjira; ndipo ena anadula nthambi za mitengo, naziyala m'njiramo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo ambirimbiri a mpingowo anayala zovala zao panjira; ndipo ena anadula nthambi za mitengo, naziyala m'njiramo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Anthu ambiri ankayala zovala zao mu mseu, ndipo ena adakadula nthambi za mitengo nkumaziyalika mumseumo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Gulu lalikulu la anthu linayala zovala zawo mu msewu pamene ena anadula nthambi zamitengo ndi kuziyala mu msewumo. Onani mutuwo |