ndipo wansembe aone, ndipo taonani, ngati nkhanambo yapitirira khungu, wansembe amutche wodetsedwa, ndilo khate.
Mateyu 15:7 - Buku Lopatulika Onyenga inu! Yesaya ananenera bwino za inu, ndi kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Onyenga inu! Yesaya ananenera bwino za inu, ndi kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu anthu achiphamaso, ndithu mneneri Yesaya adaanenadi zoona muja adaati, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Inu anthu achiphamaso, Yesaya ananenera za inu kuti, |
ndipo wansembe aone, ndipo taonani, ngati nkhanambo yapitirira khungu, wansembe amutche wodetsedwa, ndilo khate.
iyeyo sadzalemekeza atate wake. Ndipo inu mupeputsa mau a Mulungu chifukwa cha miyambo yanu.
Wonyenga iwe! Tayamba kuchotsa m'diso lako mtandawo, ndipo pomwepo udzapenyetsa kuchotsa kachitsotso m'diso la mbale wako.
Ndipo Iye ananena nao, Yesaya ananenera bwino za inu onyenga, monga mwalembedwa, Anthu awa andilemekeza Ine ndi milomo yao, koma mtima wao ukhala kutali ndi Ine.