Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 13:8 - Buku Lopatulika

8 ndipo wansembe aone, ndipo taonani, ngati nkhanambo yapitirira khungu, wansembe amutche wodetsedwa, ndilo khate.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 ndipo wansembe aone, ndipo taonani, ngati nkhanambo yapitirira khungu, wansembe amutche wodetsedwa, ndilo khate.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Wansembe amuwonetsetsenso munthuyo. Akaona kuti m'bukowo wafalikiradi pa khungu, atchule wodwalayo kuti ndi woipitsidwa, limenelo ndi khate.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Wansembe amuonetsetsenso munthuyo, ndipo ngati mʼbukowo wafalikira pa khungu, wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa ndi kuti nthendayo ndi khate.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 13:8
9 Mawu Ofanana  

Ngati munthu ali nacho chotupa, kapena nkhanambo, kapena chikanga pa khungu la thupi lake, ndipo isandulika nthenda yakhate pa khungu la thupi lake, azifika kwa Aroni wansembe, kapena kwa mmodzi wa ana ake ansembe;


ndipo wansembe aione nthenda pa khungu la thupi; ndipo ngati tsitsi la panthenda lasanduka la mbuu, ndi nthenda ikaoneka yapitirira khungu la thupi lake, ndiyo nthenda yakhate; ndipo wansembe amuone, namutche wodetsedwa.


koma nkhanambo ikapitirira khungu, atadzionetsa kwa wansembe kuti atchedwe woyera, adzionetsenso kwa wansembe;


Pamene nthenda yakhate ili mwa munthu, azimfikitsa kwa wansembe;


Uza ana a Israele kuti azitulutsa m'chigono akhate onse, ndi onse akukhala nako kukha, ndi onse odetsedwa chifukwa cha akufa;


Ulibe gawo kapena cholandira ndi mau awa; pakuti mtima wako suli wolunjika pamaso pa Mulungu.


ndi kuwalonjeza ufulu, pamene iwo eni ali akapolo a chivundi; pakuti chimene munthu agonjetsedwa nacho, adzakhala kapolo wa chimenecho.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa