Levitiko 13:7 - Buku Lopatulika7 koma nkhanambo ikapitirira khungu, atadzionetsa kwa wansembe kuti atchedwe woyera, adzionetsenso kwa wansembe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 koma nkhanambo ikapitirira khungu, atadzionetsa kwa wansembe kuti atchedwe woyera, adzionetsenso kwa wansembe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Koma m'bukowo ukafalikira pa khungu, munthuyo atadziwonetsa kale kwa wansembe kuti amuyeretse, munthuyo akaonekerenso pamaso pa wansembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma ngati mʼbukowo ufalikira pakhungu atakadzionetsa kale kwa wansembe ndipo wansembeyo nʼkulengeza kuti munthuyo ndi woyeretsedwa, ndiye kuti apitenso kukadzionetsa kwa wansembeyo. Onani mutuwo |