Levitiko 13:9 - Buku Lopatulika9 Pamene nthenda yakhate ili mwa munthu, azimfikitsa kwa wansembe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pamene nthenda yakhate ili mwa munthu, azimfikitsa kwa wansembe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Munthu akagwidwa ndi nthenda ya khate, abwere naye kwa wansembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Ngati munthu aliyense ali ndi nthenda ya pakhungu yoyipitsa thupi, wodwalayo abwere naye kwa wansembe. Onani mutuwo |