Levitiko 13:10 - Buku Lopatulika10 ndipo wansembe aone, ndipo taonani, ngati pali chotupa choyera pakhungu, ndipo chasanduliza tsitsi likhale loyera, ndipo pachotupa pali mnofu wofiira, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 ndipo wansembe aone, ndipo taonani, ngati pali chotupa choyera pakhungu, ndipo chasanduliza tsitsi likhale loyera, ndipo pachotupa pali mnofu wofiira, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Wansembe amuwonetsetse. Akakhala ndi chithupsa cha maonekedwe oyera pa khungu, chimene chasandutsa ubweya wapamalopo kukhala woyera, ndipo pachithupsapo pakakhala zilonda, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Wansembe amuonetsetse munthuyo, ndipo ngati ali ndi chithupsa chamaonekedwe woyera pa khungupo chimene chasandutsa ubweya wa pamalopo kukhala woyera, ndipo ngati pali zilonda pa chotupacho, Onani mutuwo |