Masalimo 8:9 - Buku Lopatulika Yehova, Ambuye wathu, dzina lanu liposadi nanga padziko lonse lapansi! Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Yehova, Ambuye wathu, dzina lanu liposadi nanga pa dziko lonse lapansi! Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chauta, Ambuye athu, dzina lanu ndi lotchuka pa dziko lonse lapansi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Inu Yehova, Ambuye athu, dzina lanu ndi lamphamvudi pa dziko lonse lapansi! |
Ntchito zanu zichulukadi, Yehova! Munazichita zonse mwanzeru; dziko lapansi lidzala nacho chuma chanu.
Yehova, Ambuye wathu, dzina lanu liposadi nanga padziko lonse lapansi! Inu amene munaika ulemerero wanu pa thambo la kumwamba.
Palibe wina ngati Mulungu, Yesuruni iwe, wakuyenda wokwera pathambo, kukuthandiza, ndi pa mitambo mu ukulu wake.