Masalimo 8:1 - Buku Lopatulika1 Yehova, Ambuye wathu, dzina lanu liposadi nanga padziko lonse lapansi! Inu amene munaika ulemerero wanu pa thambo la kumwamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Yehova, Ambuye wathu, dzina lanu liposadi nanga pa dziko lonse lapansi! Inu amene munaika ulemerero wanu pa thambo la kumwamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Chauta, Ambuye athu, dzina lanu ndi lotchuka pa dziko lonse lapansi. Kumwamba amaimba nyimbo zotamanda ulemerero wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Inu Yehova Ambuye athu, dzina lanu ndi la lamphamvudi pa dziko lonse lapansi! Inu mwakhazikitsa ulemerero wanu mʼmayiko onse akumwamba. Onani mutuwo |