Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Masalimo 41:8 - Buku Lopatulika

Chamgwera chinthu choopsa, ati; popeza ali gonire sadzaukanso.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Chamgwera chinthu choopsa, ati; popeza ali gonire sadzaukanso.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Amati, “Yamgwera nthenda yofa nayo, sadzukanso pamene wagonapo.”

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

“Matenda owopsa amugwira; sadzaukapo pamalo pamene wagona.”

Onani mutuwo



Masalimo 41:8
7 Mawu Ofanana  

Ambiri amati kwa moyo wanga, alibe chipulumutso mwa Mulungu.


ndi kuti, Wamsiya Mulungu. Mlondoleni, mgwireni; popeza palibe wompulumutsa.


Ndipo mkazi uyu, ndiye mwana wa Abrahamu, amene Satana anammanga, onani, zaka khumi ndi zisanu ndi zitatu, nanga si kuyenera kodi, kuti amasulidwe nsinga yake imeneyi tsiku la Sabata?