Masalimo 41:7 - Buku Lopatulika7 Onse akudana nane andinong'onezerana; apangana chondiipsa ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Onse akudana nane andinong'onezerana; apangana chondiipsa ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Onse odana nane amanong'onezana za ine, amayesa kuti zoipa zandigwera chifukwa cha kuipa kwanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Adani anga onse amanongʼonezana pamodzi kulimbana nane, iwo amalingalira zoyipa kwambiri za ine, ponena kuti, Onani mutuwo |