Masalimo 41:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo akadza kundiona wina angonena bodza; mumtima mwake adzisonkhera zopanda pake, akanka nayenda namakanena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo akadza kundiona wina angonena bodza; mumtima mwake adzisonkhera zopanda pake, akanka nayenda namakanena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Amene amabwera kudzandiwona, ndi wosakhulupirika, mumtima mwake amaganiza zoipa za ine, ndipo akatuluka, amakaziwanditsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Pamene wina abwera kudzandiona, amayankhula mwachinyengo, pomwe mtima wake ukusonkhanitsa zachipongwe; kenaka iye amatuluka ndi kukalengeza kunja. Onani mutuwo |