Masalimo 41:5 - Buku Lopatulika5 Adani anga andinenera choipa, ndi kuti, adzafa liti, ndi kutayika dzina lake? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Adani anga andinenera choipa, ndi kuti, adzafa liti, ndi kutayika dzina lake? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Koma adani anga ondifunira zoipa, amati, “Kodi munthu ameneyu adzafa liti, kuti aiŵalike?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Adani anga mwankhwidzi amanena za ine kuti, “Kodi munthu ameneyu adzafa liti kuti ayiwalike?” Onani mutuwo |